Akolose 3:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Inunso munayendapo m’zinthu zimenezi, pamene munali kukhalira kuchita zomwezo.+ Tito 3:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Pakuti ngakhale ife nthawi inayake tinali opanda nzeru, osamvera, osocheretsedwa, akapolo a zilakolako ndi zosangalatsa zosiyanasiyana, ochita zoipa, akaduka, onyansa ndiponso achidani.+
3 Pakuti ngakhale ife nthawi inayake tinali opanda nzeru, osamvera, osocheretsedwa, akapolo a zilakolako ndi zosangalatsa zosiyanasiyana, ochita zoipa, akaduka, onyansa ndiponso achidani.+