Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 32:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 Pakuti pa kukwiya kwanga moto wayaka,+

      Ndipo udzayaka mpaka kukafika ku Manda,* malo a pansi penipeni.+

      Udzanyeketsa dziko lapansi ndi zipatso zake,+

      Ndi kuyatsa maziko a mapiri.+

  • 2 Mbiri 36:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Koma iwo ankangonyogodola+ amithenga a Mulungu woona, kunyoza mawu ake+ ndi kuseka+ aneneri ake, mpaka kufika poti panalibenso chiyembekezo choti angathe kuchiritsidwa.+ Kenako mkwiyo+ wa Yehova unawagwera.

  • Yesaya 33:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Mu Ziyoni, anthu ochimwa akuchita mantha.+ Opanduka akunjenjemera kwambiri.+ Akufunsa kuti: ‘Ndani wa ife angakhale pambali pa moto wowononga?+ Ndani wa ife angakhale pafupi ndi moto woyaka kwambiri wosatherapo?’+

  • Yeremiya 7:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 Choncho Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti, ‘Taonani! Mkwiyo wanga ndi ukali wanga zikutsanulidwa pamalo awa,+ pamunthu, pachiweto, pamtengo wakuthengo,+ ndi pachipatso chilichonse chochokera m’nthaka yawo, ndipo udzayaka moti sudzazimitsidwa.’+

  • Yeremiya 17:27
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 27 “‘“Koma ngati simudzamvera mawu anga akuti muziona tsiku la sabata kukhala lopatulika ndi kuti musamanyamule katundu+ kulowa naye pazipata za Yerusalemu pa tsiku la sabata, ine ndidzatentha ndi moto zipata za mzindawu.+ Motowo udzanyeketsa nsanja zokhalamo za Yerusalemu+ ndipo sudzazimitsidwa.”’”+

  • Ezekieli 20:48
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 48 Anthu onse adzaona kuti ine Yehova ndaiyatsa moto nkhalangoyo ndipo sudzatheka kuuzimitsa.”’”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena