Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 29:28
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 28 Choncho Yehova anawazula m’dziko lawo atapsa mtima,+ ali ndi ukali ndiponso mkwiyo waukulu n’kuwataya m’dziko lina monga mmene zilili lero.’+

  • 2 Mbiri 34:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 “Pitani mukafunsire+ kwa Yehova m’malo mwa ineyo,+ ndiponso m’malo mwa anthu amene atsala mu Isiraeli ndi mu Yuda. Mukafunse zokhudza mawu a m’buku+ limene lapezekali, chifukwa mkwiyo wa Yehova+ umene akuyenera kutitsanulira ndi waukulu, popeza makolo athu sanasunge mawu a Yehova. Iwo sanachite zonse zimene zinalembedwa m’buku ili.”+

  • Salimo 74:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 74 Inu Mulungu, n’chifukwa chiyani mwatitaya?+

      N’chifukwa chiyani mkwiyo wanu ukuyakira nkhosa zimene mukuweta?+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena