Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 28:66
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 66 Pamenepo moyo wako udzakhala pangozi yaikulu koopsa, ndipo udzakhala wamantha usiku ndi usana, moti sudzakhala wotsimikiza za moyo wako.+

  • Deuteronomo 28:67
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 67 M’mawa udzanena kuti, ‘Zikanakhala bwino akanakhala madzulo!’ ndipo madzulo udzanena kuti, ‘Zikanakhala bwino ukanakhala m’mawa!’ chifukwa cha mantha amene adzagwira mtima wako, ndiponso chifukwa cha zimene maso ako adzaona.+

  • Salimo 53:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  5 Nthawi yomweyo anagwidwa ndi mantha aakulu,+

      Ngakhale kuti panalibe chochititsa mantha.+

      Pakuti Mulungu adzamwaza mafupa a aliyense womanga msasa kuti akuukireni.+

      Isiraeli adzawachititsa manyazi pakuti Yehova wawakana.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena