2 Mafumu 17:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Chotero Yehova anakana mbewu yonse+ ya Isiraeli ndipo anawasautsa n’kuwapereka m’manja mwa olanda katundu, mpaka iye anawathamangitsa pamaso pake.+ Salimo 35:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Amene akufunafuna moyo wanga achite manyazi ndi kunyozeka.+Amene akundikonzera chiwembu muwabweze ndipo athedwe nzeru.+ Yeremiya 6:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Anthu adzawatcha, ‘siliva wokanidwa,’+ pakuti Yehova wawakana.”+
20 Chotero Yehova anakana mbewu yonse+ ya Isiraeli ndipo anawasautsa n’kuwapereka m’manja mwa olanda katundu, mpaka iye anawathamangitsa pamaso pake.+
4 Amene akufunafuna moyo wanga achite manyazi ndi kunyozeka.+Amene akundikonzera chiwembu muwabweze ndipo athedwe nzeru.+