Levitiko 26:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Ine ndidzakukanani,* ndipo adani anu adzakugonjetsani+ ndi kukuponderezani,+ moti muzidzathawa popanda munthu wokuthamangitsani.+ Levitiko 26:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 “‘Ndidzaika mantha m’mitima ya otsala pakati panu+ amene ali m’dziko la adani awo, moti adzathawa m’tswatswa wa tsamba louluka, ndipo adzathawa ngati kuti akuthawa lupanga. Pamenepo adzagwa popanda munthu wowathamangitsa.+ Miyambo 28:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Anthu oipa amathawa popanda wowathamangitsa,+ koma olungama ali ngati mkango wamphamvu umene umakhala wolimba mtima.+
17 Ine ndidzakukanani,* ndipo adani anu adzakugonjetsani+ ndi kukuponderezani,+ moti muzidzathawa popanda munthu wokuthamangitsani.+
36 “‘Ndidzaika mantha m’mitima ya otsala pakati panu+ amene ali m’dziko la adani awo, moti adzathawa m’tswatswa wa tsamba louluka, ndipo adzathawa ngati kuti akuthawa lupanga. Pamenepo adzagwa popanda munthu wowathamangitsa.+
28 Anthu oipa amathawa popanda wowathamangitsa,+ koma olungama ali ngati mkango wamphamvu umene umakhala wolimba mtima.+