Salimo 106:41 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 41 Mobwerezabwereza anali kuwapereka m’manja mwa anthu a mitundu ina,+Kuti anthu odana nawo awalamulire,+ Maliro 1:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Adani ake akumulamulira.+ Anthu odana naye sakuda nkhawa.+Yehova wamuchititsa kukhala wachisoni chifukwa cha kuchuluka kwa machimo+ ake,Ndipo ana ake ayenda patsogolo pa adani awo atagwidwa ukapolo.+
41 Mobwerezabwereza anali kuwapereka m’manja mwa anthu a mitundu ina,+Kuti anthu odana nawo awalamulire,+ Maliro 1:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Adani ake akumulamulira.+ Anthu odana naye sakuda nkhawa.+Yehova wamuchititsa kukhala wachisoni chifukwa cha kuchuluka kwa machimo+ ake,Ndipo ana ake ayenda patsogolo pa adani awo atagwidwa ukapolo.+
5 Adani ake akumulamulira.+ Anthu odana naye sakuda nkhawa.+Yehova wamuchititsa kukhala wachisoni chifukwa cha kuchuluka kwa machimo+ ake,Ndipo ana ake ayenda patsogolo pa adani awo atagwidwa ukapolo.+