Nehemiya 13:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Anthu a ku Turo+ anali kukhala mumzindawo ndipo anali kubweretsa nsomba ndi malonda osiyanasiyana.+ Iwo anali kugulitsa zinthu zimenezi pa tsiku la sabata kwa ana a Yuda mu Yerusalemu.
16 Anthu a ku Turo+ anali kukhala mumzindawo ndipo anali kubweretsa nsomba ndi malonda osiyanasiyana.+ Iwo anali kugulitsa zinthu zimenezi pa tsiku la sabata kwa ana a Yuda mu Yerusalemu.