-
Nehemiya 10:31Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
31 Kunena za mitundu ya anthu a m’dzikolo+ imene inali kudzagulitsa katundu ndi mbewu zamtundu uliwonse* pa sabata, tinalumbira kuti sitigula kalikonse kuchokera kwa iwo pa sabata+ kapena pa tsiku lililonse lopatulika.+ Tinalumbiranso kuti sitiyenera kulima minda yathu m’chaka cha 7,+ ndipo tiyenera kukhululukira ngongole wina aliyense.+
-