Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 15:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 “Kumapeto kwa zaka 7 zilizonse uzilengeza kuti anthu amene anakongola zinthu zako amasuka ku ngongoleyo.

  • Deuteronomo 15:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Kumasula anthu angongoleko kuzichitika motere:+ munthu aliyense asafunse ngongole imene anabwereketsa mnzake. Asakakamize mnzake kapena m’bale wake kupereka ngongoleyo,+ chifukwa chilengezo choti anthu angongole amasuke chiyenera kuperekedwa pamaso pa Yehova.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena