Ekisodo 23:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Koma chaka cha 7 usaulime, uusiye kuti ugonere.+ Osauka mwa anthu ako adye za m’mundamo ndipo zimene iwo asiya, zilombo zakutchire zidye.+ Uzichita zimenezi ndi munda wako wa mpesa ndi wa maolivi. Levitiko 25:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Koma m’chaka cha 7 dzikolo lizisunga sabata lopuma pa zonse,+ sabata la Yehova. Musalime minda yanu, ndipo musatengulire mitengo yanu ya mpesa.
11 Koma chaka cha 7 usaulime, uusiye kuti ugonere.+ Osauka mwa anthu ako adye za m’mundamo ndipo zimene iwo asiya, zilombo zakutchire zidye.+ Uzichita zimenezi ndi munda wako wa mpesa ndi wa maolivi.
4 Koma m’chaka cha 7 dzikolo lizisunga sabata lopuma pa zonse,+ sabata la Yehova. Musalime minda yanu, ndipo musatengulire mitengo yanu ya mpesa.