Ekisodo 23:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Koma chaka cha 7 usaulime, uusiye kuti ugonere.+ Osauka mwa anthu ako adye za m’mundamo ndipo zimene iwo asiya, zilombo zakutchire zidye.+ Uzichita zimenezi ndi munda wako wa mpesa ndi wa maolivi. Levitiko 26:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 “‘Pa masiku onse amene dzikolo lidzakhala bwinja, lidzabweza masabata ake, inu muli m’dziko la adani anu. Nthawi imeneyo, dziko lidzasunga sabata ndipo lidzabweza masabata ake.+
11 Koma chaka cha 7 usaulime, uusiye kuti ugonere.+ Osauka mwa anthu ako adye za m’mundamo ndipo zimene iwo asiya, zilombo zakutchire zidye.+ Uzichita zimenezi ndi munda wako wa mpesa ndi wa maolivi.
34 “‘Pa masiku onse amene dzikolo lidzakhala bwinja, lidzabweza masabata ake, inu muli m’dziko la adani anu. Nthawi imeneyo, dziko lidzasunga sabata ndipo lidzabweza masabata ake.+