Yeremiya 20:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Mwandidabwitsa inu Yehova, ndipo ndadabwa. Mwagwiritsa ntchito mphamvu zanu pa ine ndipo mwapambana.+ Ndakhala chinthu choseketsa tsiku lonse. Aliyense akungondinyoza.+
7 Mwandidabwitsa inu Yehova, ndipo ndadabwa. Mwagwiritsa ntchito mphamvu zanu pa ine ndipo mwapambana.+ Ndakhala chinthu choseketsa tsiku lonse. Aliyense akungondinyoza.+