Ezekieli 3:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Mzimu unandinyamula+ moti ndinapita ndili wachisoni ndi wokwiya kwambiri mumtima mwanga, ndipo dzanja la Yehova linandigwira mwamphamvu.+ Mika 3:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Koma ine ndili ndi mphamvu zochuluka chifukwa cha mzimu wa Yehova. Ndine wokonzeka kuchita zachilungamo ndi kusonyeza mphamvu+ kuti ndiuze mbadwa za Yakobo za kupanduka kwawo, komanso kuti ndiuze Isiraeli za tchimo lake.+
14 Mzimu unandinyamula+ moti ndinapita ndili wachisoni ndi wokwiya kwambiri mumtima mwanga, ndipo dzanja la Yehova linandigwira mwamphamvu.+
8 Koma ine ndili ndi mphamvu zochuluka chifukwa cha mzimu wa Yehova. Ndine wokonzeka kuchita zachilungamo ndi kusonyeza mphamvu+ kuti ndiuze mbadwa za Yakobo za kupanduka kwawo, komanso kuti ndiuze Isiraeli za tchimo lake.+