Yesaya 11:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Mzimu wa Yehova udzakhazikika pa iye,+ mzimu wanzeru,+ womvetsa zinthu,+ wolangiza, wamphamvu,+ wodziwa zinthu+ ndi woopa Yehova.+ Zekariya 4:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Choncho iye anandiuza kuti: “Yehova wauza Zerubabele kuti, ‘“Kuti zinthu zonsezi zichitike, sipakufunika gulu lankhondo,+ kapena mphamvu,+ koma mzimu wanga,”+ watero Yehova wa makamu. Machitidwe 4:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Pamenepo Petulo, atadzazidwa ndi mzimu woyera,+ anawayankha kuti: “Olamulira anthu ndiponso akulu inu, 1 Akorinto 2:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Polankhula ndi polalikira, mawu anga sanali okopa, oonetsa nzeru, koma oonetsa mzimu ndi mphamvu,+
2 Mzimu wa Yehova udzakhazikika pa iye,+ mzimu wanzeru,+ womvetsa zinthu,+ wolangiza, wamphamvu,+ wodziwa zinthu+ ndi woopa Yehova.+
6 Choncho iye anandiuza kuti: “Yehova wauza Zerubabele kuti, ‘“Kuti zinthu zonsezi zichitike, sipakufunika gulu lankhondo,+ kapena mphamvu,+ koma mzimu wanga,”+ watero Yehova wa makamu.
8 Pamenepo Petulo, atadzazidwa ndi mzimu woyera,+ anawayankha kuti: “Olamulira anthu ndiponso akulu inu,