Habakuku 3:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Mapiri anakuonani ndipo anamva ululu waukulu.+ Mvula yamphamvu yamabingu inadutsa. Madzi akuya anachita mkokomo+ ndipo anathuvuka m’malere.
10 Mapiri anakuonani ndipo anamva ululu waukulu.+ Mvula yamphamvu yamabingu inadutsa. Madzi akuya anachita mkokomo+ ndipo anathuvuka m’malere.