Ekisodo 19:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Pamenepo phiri la Sinai linafuka utsi ponseponse,+ chifukwa chakuti Yehova anatsikira paphiripo m’moto.+ Utsi wakewo unali kukwera kumwamba ngati utsi wa uvuni,+ ndipo phiri lonse linali kunjenjemera kwambiri.+ Salimo 114:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Mapiri anadumphadumpha ngati nkhosa zamphongo,+Zitunda zinadumphadumpha ngati ana a nkhosa.
18 Pamenepo phiri la Sinai linafuka utsi ponseponse,+ chifukwa chakuti Yehova anatsikira paphiripo m’moto.+ Utsi wakewo unali kukwera kumwamba ngati utsi wa uvuni,+ ndipo phiri lonse linali kunjenjemera kwambiri.+