-
1 Mafumu 19:11Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
11 Koma Mulungu anati: “Tuluka, kaime paphiri pamaso pa Yehova.”+ Kenako Yehova anadutsa,+ ndipo kunawomba chimphepo champhamvu chomwe chinali kung’amba mapiri ndi kuphwanya matanthwe pamaso pa Yehova.+ (Yehova sanali mumphepoyo.) Pambuyo pa chimphepocho, kunachita chivomezi.+ (Yehova sanali m’chivomezicho.)
-