Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yobu 38:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 38 Tsopano Yehova anamuyankha Yobu kuchokera mumphepo yamkuntho+ kuti:

  • Salimo 50:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  3 Mulungu wathu adzabwera ndipo sadzakhala chete.+

      Pamaso pake pali moto wonyeketsa,+

      Ndipo pamalo onse omuzungulira pali mkuntho wamphamvu.+

  • Yesaya 29:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Yehova wa makamu adzatembenukira kwa iwe kuti akupulumutse ndi mabingu, zivomezi, phokoso lalikulu, mphepo yamkuntho, ndi lawi la moto wowononga.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena