Salimo 83:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 83 Inu Mulungu, musakhale chete.+Musakhale phee osalankhulapo kanthu ndipo musakhale duu osachitapo kanthu, inu Mulungu.+ Yesaya 42:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Yehova adzanyamuka ngati munthu wamphamvu.+ Ngati wankhondo, iye adzachita zinthu modzipereka kwambiri.+ Iye adzafuula, ndithu adzafuula mfuu yankhondo,+ ndipo adzakhala wamphamvu kuposa adani ake.+ Yesaya 65:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 “Taonani! Zalembedwa pamaso panga.+ Ine sindidzakhala chete,+ koma ndidzapereka mphoto.+ Mphotoyo ndidzaiika pachifuwa pawo,+
83 Inu Mulungu, musakhale chete.+Musakhale phee osalankhulapo kanthu ndipo musakhale duu osachitapo kanthu, inu Mulungu.+
13 Yehova adzanyamuka ngati munthu wamphamvu.+ Ngati wankhondo, iye adzachita zinthu modzipereka kwambiri.+ Iye adzafuula, ndithu adzafuula mfuu yankhondo,+ ndipo adzakhala wamphamvu kuposa adani ake.+
6 “Taonani! Zalembedwa pamaso panga.+ Ine sindidzakhala chete,+ koma ndidzapereka mphoto.+ Mphotoyo ndidzaiika pachifuwa pawo,+