Hoseya 11:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Iwo adzayenda motsatira Yehova+ amene adzabangula ngati mkango.+ Inde adzabangula,+ ndipo ana ake adzabwera akunjenjemera kuchokera kumadzulo.+ Yoweli 3:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Yehova adzabangula ngati mkango kuchokera m’Ziyoni ndipo adzalankhula ali ku Yerusalemu.+ Kumwamba ndi dziko lapansi zidzagwedezeka+ koma Yehova adzakhala chitetezo kwa anthu ake,+ ndipo adzakhala malo a chitetezo champhamvu kwa ana a Isiraeli.+
10 Iwo adzayenda motsatira Yehova+ amene adzabangula ngati mkango.+ Inde adzabangula,+ ndipo ana ake adzabwera akunjenjemera kuchokera kumadzulo.+
16 Yehova adzabangula ngati mkango kuchokera m’Ziyoni ndipo adzalankhula ali ku Yerusalemu.+ Kumwamba ndi dziko lapansi zidzagwedezeka+ koma Yehova adzakhala chitetezo kwa anthu ake,+ ndipo adzakhala malo a chitetezo champhamvu kwa ana a Isiraeli.+