Deuteronomo 32:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 Onani tsopano kuti ndine Mulungu,+Ndipo palibe milungu ina pamodzi ndi ine.+Ndimapha ndiponso ndimapereka moyo.+Ndavulaza koopsa,+ ndipo ine ndidzachiritsa,+Palibe aliyense wonditsomphola m’dzanja langa.+ 1 Samueli 2:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Onse olimbana ndi Yehova adzagwidwa ndi mantha.+Motsutsana nawo, iye adzagunda ngati mabingu kumwamba.+Yehova mwiniwake adzaweruza dziko lonse lapansi,+Kuti apereke mphamvu kwa mfumu yake,+Ndi kuti akweze nyanga ya wodzozedwa wake.”+
39 Onani tsopano kuti ndine Mulungu,+Ndipo palibe milungu ina pamodzi ndi ine.+Ndimapha ndiponso ndimapereka moyo.+Ndavulaza koopsa,+ ndipo ine ndidzachiritsa,+Palibe aliyense wonditsomphola m’dzanja langa.+
10 Onse olimbana ndi Yehova adzagwidwa ndi mantha.+Motsutsana nawo, iye adzagunda ngati mabingu kumwamba.+Yehova mwiniwake adzaweruza dziko lonse lapansi,+Kuti apereke mphamvu kwa mfumu yake,+Ndi kuti akweze nyanga ya wodzozedwa wake.”+