1 Samueli 7:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Pamene Samueli anali kupereka nsembe yopsereza, Afilisiti anayandikira kuti amenyane ndi Isiraeli. Zitatero, Yehova anachititsa mabingu amphamvu kwambiri+ pa tsiku limenelo kuti asokoneze Afilisiti.+ Choncho Afilisitiwo anagonjetsedwa pamaso pa Isiraeli.+ 2 Samueli 22:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ali kumwamba, Yehova anayamba kugunda ngati mabingu,+Wam’mwambamwamba anayamba kutulutsa mawu ake.+ Salimo 18:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Ali kumwamba, Yehova anayamba kugunda ngati mabingu,+Wam’mwambamwamba anayamba kutulutsa mawu ake,+Anatulutsanso matalala ndi makala onyeka a moto.
10 Pamene Samueli anali kupereka nsembe yopsereza, Afilisiti anayandikira kuti amenyane ndi Isiraeli. Zitatero, Yehova anachititsa mabingu amphamvu kwambiri+ pa tsiku limenelo kuti asokoneze Afilisiti.+ Choncho Afilisitiwo anagonjetsedwa pamaso pa Isiraeli.+
14 Ali kumwamba, Yehova anayamba kugunda ngati mabingu,+Wam’mwambamwamba anayamba kutulutsa mawu ake.+
13 Ali kumwamba, Yehova anayamba kugunda ngati mabingu,+Wam’mwambamwamba anayamba kutulutsa mawu ake,+Anatulutsanso matalala ndi makala onyeka a moto.