1 Samueli 2:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Onse olimbana ndi Yehova adzagwidwa ndi mantha.+Motsutsana nawo, iye adzagunda ngati mabingu kumwamba.+Yehova mwiniwake adzaweruza dziko lonse lapansi,+Kuti apereke mphamvu kwa mfumu yake,+Ndi kuti akweze nyanga ya wodzozedwa wake.”+ 2 Samueli 22:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ali kumwamba, Yehova anayamba kugunda ngati mabingu,+Wam’mwambamwamba anayamba kutulutsa mawu ake.+
10 Onse olimbana ndi Yehova adzagwidwa ndi mantha.+Motsutsana nawo, iye adzagunda ngati mabingu kumwamba.+Yehova mwiniwake adzaweruza dziko lonse lapansi,+Kuti apereke mphamvu kwa mfumu yake,+Ndi kuti akweze nyanga ya wodzozedwa wake.”+
14 Ali kumwamba, Yehova anayamba kugunda ngati mabingu,+Wam’mwambamwamba anayamba kutulutsa mawu ake.+