2 Samueli 22:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ali kumwamba, Yehova anayamba kugunda ngati mabingu,+Wam’mwambamwamba anayamba kutulutsa mawu ake.+ Salimo 29:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Liwu la Yehova lili pamwamba pa madzi,*+Liwu la Mulungu waulemerero+ lagunda ngati bingu.+Yehova ali pamwamba pa madzi ambiri.+
14 Ali kumwamba, Yehova anayamba kugunda ngati mabingu,+Wam’mwambamwamba anayamba kutulutsa mawu ake.+
3 Liwu la Yehova lili pamwamba pa madzi,*+Liwu la Mulungu waulemerero+ lagunda ngati bingu.+Yehova ali pamwamba pa madzi ambiri.+