Salimo 93:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ulemerero wa Yehova ndi waukulu+ kumwamba,Kuposa mkokomo wa madzi ambiri, kuposanso mafunde amphamvu a m’nyanja.+ Salimo 104:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Inu munamanga zipinda za m’mwamba pamadzi pogwiritsa ntchito mitanda,+Munapanga mitambo kukhala galeta lanu,+Mumayenda pamapiko a mphepo.+
4 Ulemerero wa Yehova ndi waukulu+ kumwamba,Kuposa mkokomo wa madzi ambiri, kuposanso mafunde amphamvu a m’nyanja.+
3 Inu munamanga zipinda za m’mwamba pamadzi pogwiritsa ntchito mitanda,+Munapanga mitambo kukhala galeta lanu,+Mumayenda pamapiko a mphepo.+