Salimo 65:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Iye akutontholetsa phokoso la nyanja,+Akutontholetsa phokoso la mafunde ake komanso chipwirikiti cha mitundu ya anthu.+ Salimo 89:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Nyanja ikadzaza mumailamulira.+Mafunde ake akamawinduka, inuyo mumawakhalitsa bata.+
7 Iye akutontholetsa phokoso la nyanja,+Akutontholetsa phokoso la mafunde ake komanso chipwirikiti cha mitundu ya anthu.+