Salimo 65:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Iye akutontholetsa phokoso la nyanja,+Akutontholetsa phokoso la mafunde ake komanso chipwirikiti cha mitundu ya anthu.+ Salimo 107:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Iye amachititsa mphepo yamkuntho kukhala bata,+Moti mafunde a panyanja amadekha.+
7 Iye akutontholetsa phokoso la nyanja,+Akutontholetsa phokoso la mafunde ake komanso chipwirikiti cha mitundu ya anthu.+