Salimo 89:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Nyanja ikadzaza mumailamulira.+Mafunde ake akamawinduka, inuyo mumawakhalitsa bata.+ Salimo 107:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Iye amachititsa mphepo yamkuntho kukhala bata,+Moti mafunde a panyanja amadekha.+