Deuteronomo 33:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Palibe wina wofanana ndi Mulungu woona+ wa Yesuruni,+Amene amayenda m’mlengalenga pokuthandiza,+Amene amayenda pamitambo mu ulemerero wake.+ Yesaya 19:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Uwu ndi uthenga wokhudza Iguputo:+ Taonani! Yehova wakwera mtambo wothamanga+ ndipo akubwera mu Iguputo. Milungu yopanda pake ya ku Iguputo idzanjenjemera chifukwa chomuopa+ ndipo mitima ya Aiguputo idzasungunuka mkati mwa dzikolo.+
26 Palibe wina wofanana ndi Mulungu woona+ wa Yesuruni,+Amene amayenda m’mlengalenga pokuthandiza,+Amene amayenda pamitambo mu ulemerero wake.+
19 Uwu ndi uthenga wokhudza Iguputo:+ Taonani! Yehova wakwera mtambo wothamanga+ ndipo akubwera mu Iguputo. Milungu yopanda pake ya ku Iguputo idzanjenjemera chifukwa chomuopa+ ndipo mitima ya Aiguputo idzasungunuka mkati mwa dzikolo.+