Yesaya 19:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Uwu ndi uthenga wokhudza Iguputo:+ Taonani! Yehova wakwera mtambo wothamanga ndipo akubwera mu Iguputo. Milungu yopanda pake ya ku Iguputo idzanjenjemera pamaso pake,+Ndipo mitima ya anthu a ku Iguputo idzachita mantha kwambiri. Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 19:1 Yesaya 1, tsa. 201
19 Uwu ndi uthenga wokhudza Iguputo:+ Taonani! Yehova wakwera mtambo wothamanga ndipo akubwera mu Iguputo. Milungu yopanda pake ya ku Iguputo idzanjenjemera pamaso pake,+Ndipo mitima ya anthu a ku Iguputo idzachita mantha kwambiri.