Yeremiya 25:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Ndinamwetsanso Farao mfumu ya Iguputo, atumiki ake, akalonga ake ndi anthu ake onse,+ Ezekieli 29:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Iwe mwana wa munthu, yang’ana kwa Farao mfumu ya Iguputo+ ndipo ulosere zoipa zimene zidzachitikire iyeyo ndi dziko lonse la Iguputo.+ Yoweli 3:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Iguputo adzasanduka bwinja,+ Edomu adzasanduka chipululu chopanda kanthu+ chifukwa cha chiwawa chimene anachitira ana a Yuda, ndiponso chifukwa chokhetsa magazi osalakwa m’dziko la Yudalo.+
2 “Iwe mwana wa munthu, yang’ana kwa Farao mfumu ya Iguputo+ ndipo ulosere zoipa zimene zidzachitikire iyeyo ndi dziko lonse la Iguputo.+
19 Iguputo adzasanduka bwinja,+ Edomu adzasanduka chipululu chopanda kanthu+ chifukwa cha chiwawa chimene anachitira ana a Yuda, ndiponso chifukwa chokhetsa magazi osalakwa m’dziko la Yudalo.+