Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yesaya 19:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Uwu ndi uthenga wokhudza Iguputo:+ Taonani! Yehova wakwera mtambo wothamanga+ ndipo akubwera mu Iguputo. Milungu yopanda pake ya ku Iguputo idzanjenjemera chifukwa chomuopa+ ndipo mitima ya Aiguputo idzasungunuka mkati mwa dzikolo.+

  • Yeremiya 25:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Ndinamwetsanso Farao mfumu ya Iguputo, atumiki ake, akalonga ake ndi anthu ake onse,+

  • Yeremiya 43:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Nebukadirezara adzabwera kudzathira nkhondo dziko la Iguputo.+ Woyenera kufa ndi mliri adzafa ndi mliri. Woyenera kutengedwa kupita ku ukapolo adzatengedwa kupita ku ukapolo. Woyenera kufa ndi lupanga adzafa ndi lupanga.+

  • Ezekieli 31:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 “Iwe mwana wa munthu, uza Farao mfumu ya Iguputo ndi khamu lake kuti,+

      “‘Kodi wakula kufanana ndi ndani?

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena