Deuteronomo 33:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Palibe wina wofanana ndi Mulungu woona+ wa Yesuruni,+Amene amayenda m’mlengalenga pokuthandiza,+Amene amayenda pamitambo mu ulemerero wake.+ Salimo 68:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Imbirani Iye wokwera kumwamba kwa kumwamba kwakale.+Tamverani! Iye akulankhula ndi mawu amphamvu.+
26 Palibe wina wofanana ndi Mulungu woona+ wa Yesuruni,+Amene amayenda m’mlengalenga pokuthandiza,+Amene amayenda pamitambo mu ulemerero wake.+
33 Imbirani Iye wokwera kumwamba kwa kumwamba kwakale.+Tamverani! Iye akulankhula ndi mawu amphamvu.+