Salimo 18:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Iye anafika atakwera pakerubi wouluka.+Mulungu anali kuuluka mwaliwiro pamapiko a cholengedwa chauzimu.*+ Salimo 104:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Inu munamanga zipinda za m’mwamba pamadzi pogwiritsa ntchito mitanda,+Munapanga mitambo kukhala galeta lanu,+Mumayenda pamapiko a mphepo.+
10 Iye anafika atakwera pakerubi wouluka.+Mulungu anali kuuluka mwaliwiro pamapiko a cholengedwa chauzimu.*+
3 Inu munamanga zipinda za m’mwamba pamadzi pogwiritsa ntchito mitanda,+Munapanga mitambo kukhala galeta lanu,+Mumayenda pamapiko a mphepo.+