-
Salimo 104:3Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
3 Inu munamanga zipinda za m’mwamba pamadzi pogwiritsa ntchito mitanda,+
Munapanga mitambo kukhala galeta lanu,+
Mumayenda pamapiko a mphepo.+
-