Salimo 104:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Inu mumapanga angelo anu kukhala mizimu,+Ndipo atumiki anu kukhala moto wonyeketsa.+