1 Mafumu 22:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Pomalizira pake, mzimu wina+ unabwera kudzaima pamaso pa Yehova n’kunena kuti, ‘Ine ndikam’pusitsa.’ Ndipo Yehova anamufunsa kuti, ‘Ukam’pusitsa motani?’+ Aheberi 1:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ndiponso ponena za angelo, iye akuti: “Amapanga angelo ake kukhala mizimu, ndipo amapanganso antchito ake otumikira ena kukhala lawi la moto.”+
21 Pomalizira pake, mzimu wina+ unabwera kudzaima pamaso pa Yehova n’kunena kuti, ‘Ine ndikam’pusitsa.’ Ndipo Yehova anamufunsa kuti, ‘Ukam’pusitsa motani?’+
7 Ndiponso ponena za angelo, iye akuti: “Amapanga angelo ake kukhala mizimu, ndipo amapanganso antchito ake otumikira ena kukhala lawi la moto.”+