Ezekieli 1:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Zamoyozo zinali zooneka ngati makala oyaka moto.+ Pakati pa zamoyozo panali zinazake zooneka ngati miyuni ya moto+ zimene zinali kuyenda uku ndi uku. Motowo unali wowala, ndipo m’motowo munali kutuluka mphezi.+ Aheberi 1:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Kodi angelo onse si mizimu+ yotumikira ena,+ yotumidwa kukatumikira amene adzalandire chipulumutso monga cholowa chawo?+
13 Zamoyozo zinali zooneka ngati makala oyaka moto.+ Pakati pa zamoyozo panali zinazake zooneka ngati miyuni ya moto+ zimene zinali kuyenda uku ndi uku. Motowo unali wowala, ndipo m’motowo munali kutuluka mphezi.+
14 Kodi angelo onse si mizimu+ yotumikira ena,+ yotumidwa kukatumikira amene adzalandire chipulumutso monga cholowa chawo?+