Salimo 104:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Inu mumapanga angelo anu kukhala mizimu,+Ndipo atumiki anu kukhala moto wonyeketsa.+ Machitidwe 23:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Pakuti Asaduki+ amanena kuti akufa sadzauka,+ kulibe angelo, kapena cholengedwa chauzimu, koma Afarisi amavomereza poyera kuti zonsezi zilipo.
8 Pakuti Asaduki+ amanena kuti akufa sadzauka,+ kulibe angelo, kapena cholengedwa chauzimu, koma Afarisi amavomereza poyera kuti zonsezi zilipo.