Ezekieli 1:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Angelowo ankaoneka ngati makala oyaka moto. Pakati pa angelowo panali zinazake zooneka ngati miyuni ya moto wowala imene inkayenda kuchokera kwa mngelo wina kupita kwa mngelo wina ndipo mʼmotowo munkatuluka mphezi.+
13 Angelowo ankaoneka ngati makala oyaka moto. Pakati pa angelowo panali zinazake zooneka ngati miyuni ya moto wowala imene inkayenda kuchokera kwa mngelo wina kupita kwa mngelo wina ndipo mʼmotowo munkatuluka mphezi.+