Ezekieli 1:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Zamoyozo zinali zooneka ngati makala oyaka moto.+ Pakati pa zamoyozo panali zinazake zooneka ngati miyuni ya moto+ zimene zinali kuyenda uku ndi uku. Motowo unali wowala, ndipo m’motowo munali kutuluka mphezi.+
13 Zamoyozo zinali zooneka ngati makala oyaka moto.+ Pakati pa zamoyozo panali zinazake zooneka ngati miyuni ya moto+ zimene zinali kuyenda uku ndi uku. Motowo unali wowala, ndipo m’motowo munali kutuluka mphezi.+