Salimo 97:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Patsogolo pake pakuyaka moto,+Ndipo ukupsereza adani ake onse omuzungulira.+