Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 34:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  7 Mngelo wa Yehova amamanga msasa mozungulira onse oopa Mulungu,+

      Ndipo amawapulumutsa.+

  • Salimo 91:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Pakuti adzalamula angelo ake za iwe,+

      Kuti akuteteze m’njira zako zonse.+

  • Mateyu 18:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Samalani anthu inu kuti musanyoze mmodzi wa tianati, chifukwa ndikukutsimikizirani kuti angelo awo+ kumwamba amaona nkhope ya Atate wanga wakumwamba nthawi zonse.+

  • Luka 2:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Mwadzidzidzi mngelo wa Yehova+ anaima chapafupi ndi iwo, ndipo ulemerero wa Yehova+ unawawalira ponsepo, mwakuti anachita mantha kwambiri.

  • Luka 2:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Mwadzidzidzi, panaoneka khamu lalikulu lakumwamba+ pamodzi ndi mngeloyo, likutamanda Mulungu+ kuti:

  • Machitidwe 5:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Koma usiku, mngelo wa Yehova+ anatsegula zitseko za ndendeyo+ ndi kuwatulutsa, ndipo anawauza kuti:

  • Machitidwe 12:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Mwadzidzidzi, mngelo wa Yehova anaimirira+ chapafupi, ndipo kuwala kunaunika m’chipinda cha ndendecho. Kenako mngeloyo anadzutsa Petulo mwa kumugunda m’nthiti,+ n’kunena kuti: “Dzuka msanga!” Pamenepo maunyolo amene anamumanga nawo manjawo anagwa pansi.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena