Machitidwe 5:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Koma usiku, mngelo wa Yehova* anatsegula zitseko za ndendeyo nʼkuwatulutsa,+ ndipo anawauza kuti: Machitidwe Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 5:19 Kuchitira Umboni Mokwanira, tsa. 38