Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Mafumu 6:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Kenako Elisa anayamba kupemphera+ kuti: “Inu Yehova, m’tseguleni maso+ chonde kuti aone.” Nthawi yomweyo Yehova anatsegula maso a mtumiki uja, moti anaona kuti dera lonse lamapiri kuzungulira Elisa+ linadzaza ndi mahatchi ndi magaleta ankhondo+ oyaka moto.

  • Salimo 91:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Pakuti adzalamula angelo ake za iwe,+

      Kuti akuteteze m’njira zako zonse.+

  • Mateyu 18:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Samalani anthu inu kuti musanyoze mmodzi wa tianati, chifukwa ndikukutsimikizirani kuti angelo awo+ kumwamba amaona nkhope ya Atate wanga wakumwamba nthawi zonse.+

  • Machitidwe 5:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Koma usiku, mngelo wa Yehova+ anatsegula zitseko za ndendeyo+ ndi kuwatulutsa, ndipo anawauza kuti:

  • Machitidwe 12:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Koma Petulo nzeru zitamubwerera, anati: “Ndadziwa tsopano kuti Yehova ndiye watumiza mngelo wake+ kudzandilanditsa+ m’manja mwa Herode, komanso kudzandilanditsa ku zonse zimene anthu achiyuda anali kuyembekezera.”

  • Aheberi 1:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Kodi angelo onse si mizimu+ yotumikira ena,+ yotumidwa kukatumikira amene adzalandire chipulumutso monga cholowa chawo?+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena