Salimo 34:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Mngelo wa Yehova amamanga msasa mozungulira onse oopa Mulungu,+Ndipo amawapulumutsa.+ Mateyu 26:53 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 53 Kapena ukuganiza kuti sindingapemphe Atate wanga kuti anditumizire magulu ankhondo oposa 12 a angelo nthawi yomwe ino?+
53 Kapena ukuganiza kuti sindingapemphe Atate wanga kuti anditumizire magulu ankhondo oposa 12 a angelo nthawi yomwe ino?+