Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 34:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  7 Mngelo wa Yehova amamanga msasa mozungulira onse oopa Mulungu,+

      Ndipo amawapulumutsa.+

  • Danieli 3:28
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 28 Pamenepo Nebukadinezara anati: “Atamandike Mulungu wa Sadirake, Mesake ndi Abedinego+ amene anatumiza mngelo wake+ ndi kupulumutsa atumiki ake amene anamudalira+ ndiponso amene sanamvere mawu a mfumu, koma anali okonzeka kufa chifukwa sanafune kutumikira+ ndi kulambira+ mulungu wina aliyense kupatulapo Mulungu wawo.+

  • Danieli 6:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 Mulungu wanga+ watumiza mngelo wake+ kudzatseka pakamwa pa mikango.+ Chotero mikangoyo sinandivulaze, chifukwa iye sanandipeze ndi mlandu uliwonse+ ndiponso sindinakulakwireni chilichonse inu mfumu.”+

  • Aheberi 1:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Kodi angelo onse si mizimu+ yotumikira ena,+ yotumidwa kukatumikira amene adzalandire chipulumutso monga cholowa chawo?+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena