Aroma 13:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Munthu aliyense azimvera+ olamulira akuluakulu,+ chifukwa palibe ulamuliro+ umene ungakhalepo kupatulapo ngati Mulungu waulola.+ Olamulira amene alipowa ali m’malo awo osiyanasiyana+ mololedwa ndi Mulungu.+ 1 Petulo 2:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Lemekezani anthu, kaya akhale amtundu wotani.+ Kondani gulu lonse la abale,+ opani Mulungu,+ lemekezani mfumu.+
13 Munthu aliyense azimvera+ olamulira akuluakulu,+ chifukwa palibe ulamuliro+ umene ungakhalepo kupatulapo ngati Mulungu waulola.+ Olamulira amene alipowa ali m’malo awo osiyanasiyana+ mololedwa ndi Mulungu.+
17 Lemekezani anthu, kaya akhale amtundu wotani.+ Kondani gulu lonse la abale,+ opani Mulungu,+ lemekezani mfumu.+