1 Yohane 2:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Amene amakonda m’bale wake ndiye kuti ali m’kuunika,+ ndipo palibe chimene chingamukhumudwitse.+ 1 Yohane 4:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Ndipo iye anatipatsa lamulo ili lakuti,+ munthu amene amakonda Mulungu azikondanso m’bale wake.+